Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 42 - المَائدة - Page - Juz 6
﴿سَمَّٰعُونَ لِلۡكَذِبِ أَكَّٰلُونَ لِلسُّحۡتِۚ فَإِن جَآءُوكَ فَٱحۡكُم بَيۡنَهُمۡ أَوۡ أَعۡرِضۡ عَنۡهُمۡۖ وَإِن تُعۡرِضۡ عَنۡهُمۡ فَلَن يَضُرُّوكَ شَيۡـٔٗاۖ وَإِنۡ حَكَمۡتَ فَٱحۡكُم بَيۡنَهُم بِٱلۡقِسۡطِۚ إِنَّ ٱللَّهَ يُحِبُّ ٱلۡمُقۡسِطِينَ ﴾
[المَائدة: 42]
﴿سماعون للكذب أكالون للسحت فإن جاءوك فاحكم بينهم أو أعرض عنهم وإن﴾ [المَائدة: 42]
Khaled Ibrahim Betala “Okonda kumvetsera zabodza; osaopa pakudya (zinthu) zoletsedwa (zaharamu). Choncho akakudzera aweruze pakati pawo, kapena uwapatukire. Ndipo ngati uwapatukira, palibe chomwe angakuvutitse nacho. Ngati uweruza pakati pawo weruza mwachilungamo. Ndithudi, Allah amakonda olungama |