×

Kodi iwo abwera bwanji kwa iwe kudzaweruzidwa pamene iwo ali ndi Buku 5:43 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:43) ayat 43 in Chichewa

5:43 Surah Al-Ma’idah ayat 43 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 43 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿وَكَيۡفَ يُحَكِّمُونَكَ وَعِندَهُمُ ٱلتَّوۡرَىٰةُ فِيهَا حُكۡمُ ٱللَّهِ ثُمَّ يَتَوَلَّوۡنَ مِنۢ بَعۡدِ ذَٰلِكَۚ وَمَآ أُوْلَٰٓئِكَ بِٱلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[المَائدة: 43]

Kodi iwo abwera bwanji kwa iwe kudzaweruzidwa pamene iwo ali ndi Buku la chipangano chakale limene muli chiweruzo cha Mulungu? Ndipo ngakhale zili tero iwo amatembenuka. Iwo si okhulupirira enieni

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وكيف يحكمونك وعندهم التوراة فيها حكم الله ثم يتولون من بعد ذلك, باللغة نيانجا

﴿وكيف يحكمونك وعندهم التوراة فيها حكم الله ثم يتولون من بعد ذلك﴾ [المَائدة: 43]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi angakuyese muweruzi chotani pomwe iwo alinayo Taurat momwe muli chiweruzo cha Allah. Pambuyo powaweruza akutembenuka (monyoza)! Ndipo iwo sali okhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek