×

Kodi ndi malamulo a chikunja amene iwo afuna kuti aweruzidwe nawo? Kodi 5:50 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:50) ayat 50 in Chichewa

5:50 Surah Al-Ma’idah ayat 50 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 50 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿أَفَحُكۡمَ ٱلۡجَٰهِلِيَّةِ يَبۡغُونَۚ وَمَنۡ أَحۡسَنُ مِنَ ٱللَّهِ حُكۡمٗا لِّقَوۡمٖ يُوقِنُونَ ﴾
[المَائدة: 50]

Kodi ndi malamulo a chikunja amene iwo afuna kuti aweruzidwe nawo? Kodi woweruza wabwino kwambiri ndani woposa Mulungu kwa anthu amene ali ndi chikhulupiriro cholimba

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أفحكم الجاهلية يبغون ومن أحسن من الله حكما لقوم يوقنون, باللغة نيانجا

﴿أفحكم الجاهلية يبغون ومن أحسن من الله حكما لقوم يوقنون﴾ [المَائدة: 50]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi iwo akufuna chiweruzo cha nthawi yaumbuli (chamasiku aumbuli, Chisilamu chisanadze)? Kodi ndani ali wabwino poweruza kuposa Allah kwa anthu otsimikiza (kuti Allah alipo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek