×

Oh iwe Mtumwi! Lalikira zimene zavumbulutsidwa kwa iwe kuchokera kwa Ambuye wako. 5:67 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:67) ayat 67 in Chichewa

5:67 Surah Al-Ma’idah ayat 67 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 67 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿۞ يَٰٓأَيُّهَا ٱلرَّسُولُ بَلِّغۡ مَآ أُنزِلَ إِلَيۡكَ مِن رَّبِّكَۖ وَإِن لَّمۡ تَفۡعَلۡ فَمَا بَلَّغۡتَ رِسَالَتَهُۥۚ وَٱللَّهُ يَعۡصِمُكَ مِنَ ٱلنَّاسِۗ إِنَّ ٱللَّهَ لَا يَهۡدِي ٱلۡقَوۡمَ ٱلۡكَٰفِرِينَ ﴾
[المَائدة: 67]

Oh iwe Mtumwi! Lalikira zimene zavumbulutsidwa kwa iwe kuchokera kwa Ambuye wako. Ndipo ngati iwe siutero, ndithudi, iwe walephera kupereka uthenga wake. Mulungu adzakuteteza iwe kwa anthu. Ndithudi Mulungu satsogolera anthu osakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الرسول بلغ ما أنـزل إليك من ربك وإن لم تفعل فما, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الرسول بلغ ما أنـزل إليك من ربك وإن لم تفعل فما﴾ [المَائدة: 67]

Khaled Ibrahim Betala
“E iwe Mtumiki! Fikitsa (kwa anthu) zomwe zavumbulutsidwa kwa iwe kuchokera kwa Mbuye wako. Ngati suchita, ndiye kuti sudafikitse uthenga Wake. Ndipo Allah akuteteza kwa anthu; (usaope aliyense). Ndithudi, Allah satsogolera anthu osakhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek