×

Oh inu anthu okhulupirira! Zoledzeretsa, masewera a mwayi, kupembedza mafano ndi mipaliro 5:90 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:90) ayat 90 in Chichewa

5:90 Surah Al-Ma’idah ayat 90 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 90 - المَائدة - Page - Juz 7

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُوٓاْ إِنَّمَا ٱلۡخَمۡرُ وَٱلۡمَيۡسِرُ وَٱلۡأَنصَابُ وَٱلۡأَزۡلَٰمُ رِجۡسٞ مِّنۡ عَمَلِ ٱلشَّيۡطَٰنِ فَٱجۡتَنِبُوهُ لَعَلَّكُمۡ تُفۡلِحُونَ ﴾
[المَائدة: 90]

Oh inu anthu okhulupirira! Zoledzeretsa, masewera a mwayi, kupembedza mafano ndi mipaliro ndi ntchito zoipa zopangidwa ndi Satana. Motero zipeweni kuti mukhale opambana

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا إنما الخمر والميسر والأنصاب والأزلام رجس من عمل الشيطان, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا إنما الخمر والميسر والأنصاب والأزلام رجس من عمل الشيطان﴾ [المَائدة: 90]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Ndithudi, mowa (kutchova) njuga, kupembedza mafano ndi kuombeza maula, (zonsezi) ndi uve, mwa ntchito za satana. Choncho zipeweni kuti mupambane
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek