×

Ndipo mverani Mulungu ndi Mtumwi. Chenjerani ndipo opani Mulungu. Ngati inu mutembenuka 5:92 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:92) ayat 92 in Chichewa

5:92 Surah Al-Ma’idah ayat 92 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 92 - المَائدة - Page - Juz 7

﴿وَأَطِيعُواْ ٱللَّهَ وَأَطِيعُواْ ٱلرَّسُولَ وَٱحۡذَرُواْۚ فَإِن تَوَلَّيۡتُمۡ فَٱعۡلَمُوٓاْ أَنَّمَا عَلَىٰ رَسُولِنَا ٱلۡبَلَٰغُ ٱلۡمُبِينُ ﴾
[المَائدة: 92]

Ndipo mverani Mulungu ndi Mtumwi. Chenjerani ndipo opani Mulungu. Ngati inu mutembenuka dziwani kuti udindo wa Mtumwi wathu ndi kupereka uthenga momveka

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأطيعوا الله وأطيعوا الرسول واحذروا فإن توليتم فاعلموا أنما على رسولنا البلاغ, باللغة نيانجا

﴿وأطيعوا الله وأطيعوا الرسول واحذروا فإن توليتم فاعلموا أنما على رسولنا البلاغ﴾ [المَائدة: 92]

Khaled Ibrahim Betala
“Mverani Allah, ndipo mverani Mtumiki ndipo chenjerani (musanyoze malamulo a Allah). Ngati munyoza, dziwani kuti udindo wa Mtumiki Wathu ndikufikitsa uthenga woonekera basi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek