×

Chakudya cha akapolo. Ndipo Ife timapereka moyo kunthaka imene idali yakufa. Kumeneko 50:11 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Qaf ⮕ (50:11) ayat 11 in Chichewa

50:11 Surah Qaf ayat 11 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Qaf ayat 11 - قٓ - Page - Juz 26

﴿رِّزۡقٗا لِّلۡعِبَادِۖ وَأَحۡيَيۡنَا بِهِۦ بَلۡدَةٗ مَّيۡتٗاۚ كَذَٰلِكَ ٱلۡخُرُوجُ ﴾
[قٓ: 11]

Chakudya cha akapolo. Ndipo Ife timapereka moyo kunthaka imene idali yakufa. Kumeneko ndiko kuuka kwa akufa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: رزقا للعباد وأحيينا به بلدة ميتا كذلك الخروج, باللغة نيانجا

﴿رزقا للعباد وأحيينا به بلدة ميتا كذلك الخروج﴾ [قٓ: 11]

Khaled Ibrahim Betala
“(Kuti chikhale) chakudya cha akapolo (a Allah); ndi madziwo taukitsa dziko lakufa (louma). Momwemo ndimmene kudzakhalira kutuluka m’manda (muli moyo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek