Quran with Chichewa translation - Surah Qaf ayat 33 - قٓ - Page - Juz 26
﴿مَّنۡ خَشِيَ ٱلرَّحۡمَٰنَ بِٱلۡغَيۡبِ وَجَآءَ بِقَلۡبٖ مُّنِيبٍ ﴾
[قٓ: 33]
﴿من خشي الرحمن بالغيب وجاء بقلب منيب﴾ [قٓ: 33]
Khaled Ibrahim Betala “Amene adaopa (Allah), Wachifundo chambiri, pomwe samamuona ndi maso, ndipo adadza ndi mtima wotembenukira (kwa Iye).” |