Quran with Chichewa translation - Surah Adh-Dhariyat ayat 29 - الذَّاريَات - Page - Juz 26
﴿فَأَقۡبَلَتِ ٱمۡرَأَتُهُۥ فِي صَرَّةٖ فَصَكَّتۡ وَجۡهَهَا وَقَالَتۡ عَجُوزٌ عَقِيمٞ ﴾
[الذَّاريَات: 29]
﴿فأقبلت امرأته في صرة فصكت وجهها وقالت عجوز عقيم﴾ [الذَّاريَات: 29]
Khaled Ibrahim Betala “Adadza mkazi wake ndi mkuwe (pamene adamva nkhani yabwino ija). Adadzimenya kunkhope (ndi dzanja lake kusonyeza kudabwa ndi kusatheka). Ndipo adati: (“Ine ndine) nkhalamba (ndiponso) chumba; (ndingabereke bwanji)?” |