Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qamar ayat 15 - القَمَر - Page - Juz 27
﴿وَلَقَد تَّرَكۡنَٰهَآ ءَايَةٗ فَهَلۡ مِن مُّدَّكِرٖ ﴾
[القَمَر: 15]
﴿ولقد تركناها آية فهل من مدكر﴾ [القَمَر: 15]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu tidachisiya (chigumula) kukhala phunziro (pakuonongeka kwa osakhulupirira ndi kupulumuka kwa okhulupirira). Kodi alipo wolikumbukira (ndi kupeza nalo malango abwino) |