Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rahman ayat 29 - الرَّحمٰن - Page - Juz 27
﴿يَسۡـَٔلُهُۥ مَن فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۚ كُلَّ يَوۡمٍ هُوَ فِي شَأۡنٖ ﴾
[الرَّحمٰن: 29]
﴿يسأله من في السموات والأرض كل يوم هو في شأن﴾ [الرَّحمٰن: 29]
Khaled Ibrahim Betala “(Onse) akumwamba ndi pansi akupempha Iye (zofuna zawo)! Tsiku lililonse Iye ali ndi zochita (monga kupatsa uyu ulemelero, ndi kutsitsa uyu) |