Quran with Chichewa translation - Surah Al-hadid ayat 12 - الحدِيد - Page - Juz 27
﴿يَوۡمَ تَرَى ٱلۡمُؤۡمِنِينَ وَٱلۡمُؤۡمِنَٰتِ يَسۡعَىٰ نُورُهُم بَيۡنَ أَيۡدِيهِمۡ وَبِأَيۡمَٰنِهِمۖ بُشۡرَىٰكُمُ ٱلۡيَوۡمَ جَنَّٰتٞ تَجۡرِي مِن تَحۡتِهَا ٱلۡأَنۡهَٰرُ خَٰلِدِينَ فِيهَاۚ ذَٰلِكَ هُوَ ٱلۡفَوۡزُ ٱلۡعَظِيمُ ﴾
[الحدِيد: 12]
﴿يوم ترى المؤمنين والمؤمنات يسعى نورهم بين أيديهم وبأيمانهم بشراكم اليوم جنات﴾ [الحدِيد: 12]
Khaled Ibrahim Betala “Tsiku limene udzaona okhulupirira aamuna ndi aakazi dangalira lawo likuyenda patsogolo pawo ndi mbali ya kumanja kwao (uku angelo akunena kwa iwo): “Chisangalalo chanu lero ndi minda imene pansi pake pakuyenda mitsinje. Mukhala m’menemo nthawi yaitali! Kumeneku ndiko kupambana kwakukulu (kwa inu) |