Quran with Chichewa translation - Surah Al-hadid ayat 13 - الحدِيد - Page - Juz 27
﴿يَوۡمَ يَقُولُ ٱلۡمُنَٰفِقُونَ وَٱلۡمُنَٰفِقَٰتُ لِلَّذِينَ ءَامَنُواْ ٱنظُرُونَا نَقۡتَبِسۡ مِن نُّورِكُمۡ قِيلَ ٱرۡجِعُواْ وَرَآءَكُمۡ فَٱلۡتَمِسُواْ نُورٗاۖ فَضُرِبَ بَيۡنَهُم بِسُورٖ لَّهُۥ بَابُۢ بَاطِنُهُۥ فِيهِ ٱلرَّحۡمَةُ وَظَٰهِرُهُۥ مِن قِبَلِهِ ٱلۡعَذَابُ ﴾
[الحدِيد: 13]
﴿يوم يقول المنافقون والمنافقات للذين آمنوا انظرونا نقتبس من نوركم قيل ارجعوا﴾ [الحدِيد: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Tsiku limene achinyengo aamuna ndi achinyengo aakazi adzauza okhulupirira (kuti:) “Tidikireni kuti tipeze kuunika kwanu!” Kudzanenedwa (mwachipongwe): “Bwererani pambuyo panu mukafune kuunika kumeneko!” Choncho padzaikidwa mpanda pakati pawo (okhulupirira ndi achinyengo) umene udzakhala ndi khomo, mkati mwake muli chifundo ndi mtendere; kunja kwake kuli mazunzo ndi chilango |