Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mujadilah ayat 21 - المُجَادلة - Page - Juz 28
﴿كَتَبَ ٱللَّهُ لَأَغۡلِبَنَّ أَنَا۠ وَرُسُلِيٓۚ إِنَّ ٱللَّهَ قَوِيٌّ عَزِيزٞ ﴾
[المُجَادلة: 21]
﴿كتب الله لأغلبن أنا ورسلي إن الله قوي عزيز﴾ [المُجَادلة: 21]
Khaled Ibrahim Betala “Allah adalamula (kuti): “Ndithu ndipambana Ine ndi atumiki Anga.” Ndithu Allah ndiwanyonga zokwana, Wopambana (sapambanidwa ndi aliyense) |