×

Ndipo iwo amene adadza pambuyo pawo adati: “Ambuye wathu, tikhululukireni ife pamodzi 59:10 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hashr ⮕ (59:10) ayat 10 in Chichewa

59:10 Surah Al-hashr ayat 10 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 10 - الحَشر - Page - Juz 28

﴿وَٱلَّذِينَ جَآءُو مِنۢ بَعۡدِهِمۡ يَقُولُونَ رَبَّنَا ٱغۡفِرۡ لَنَا وَلِإِخۡوَٰنِنَا ٱلَّذِينَ سَبَقُونَا بِٱلۡإِيمَٰنِ وَلَا تَجۡعَلۡ فِي قُلُوبِنَا غِلّٗا لِّلَّذِينَ ءَامَنُواْ رَبَّنَآ إِنَّكَ رَءُوفٞ رَّحِيمٌ ﴾
[الحَشر: 10]

Ndipo iwo amene adadza pambuyo pawo adati: “Ambuye wathu, tikhululukireni ife pamodzi ndi abale athu amene adalowa Chisilamu poyambirira, ndipo musasiye m’mitima mwathu kaduka wowachitira iwo amene adakhulupirira kale. Ambuye wathu! Ndithudi inu ndinu okoma mtima, Mwini chifundo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين جاءوا من بعدهم يقولون ربنا اغفر لنا ولإخواننا الذين سبقونا بالإيمان, باللغة نيانجا

﴿والذين جاءوا من بعدهم يقولون ربنا اغفر لنا ولإخواننا الذين سبقونا بالإيمان﴾ [الحَشر: 10]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (okhulupirira) amene adadza pambuyo (pa Amuhajirina ndi Answari) akunena kuti: “Mbuye wathu tikhululukireni ndi anzathu amene adatitsogolera pa chikhulupiliro, ndipo musaike m’mitima mwathu njiru ndi chidani kwa amene adakhulupirira. E Mbuye wathu! Inu ndinu Wodekha, Wachisoni chosatha.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek