×

Kodi iwe sudawaone anthu a chinyengo ali kunena kwa abale awo osakhulupirira 59:11 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hashr ⮕ (59:11) ayat 11 in Chichewa

59:11 Surah Al-hashr ayat 11 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 11 - الحَشر - Page - Juz 28

﴿۞ أَلَمۡ تَرَ إِلَى ٱلَّذِينَ نَافَقُواْ يَقُولُونَ لِإِخۡوَٰنِهِمُ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ مِنۡ أَهۡلِ ٱلۡكِتَٰبِ لَئِنۡ أُخۡرِجۡتُمۡ لَنَخۡرُجَنَّ مَعَكُمۡ وَلَا نُطِيعُ فِيكُمۡ أَحَدًا أَبَدٗا وَإِن قُوتِلۡتُمۡ لَنَنصُرَنَّكُمۡ وَٱللَّهُ يَشۡهَدُ إِنَّهُمۡ لَكَٰذِبُونَ ﴾
[الحَشر: 11]

Kodi iwe sudawaone anthu a chinyengo ali kunena kwa abale awo osakhulupirira amene ali pakati pa anthu a m’Buku? (Ponena kuti): “Ngati iwo akupirikitsani inu, nafenso tidzapita nanu, ndipo sitidzamvera wina aliyense wodana ndi inu. Ngati inu muputidwa, ndithudi, ife tidzakuthandizani.” Koma Mulungu achitira umboni kuti, ndithudi, iwo ndi abodza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ألم تر إلى الذين نافقوا يقولون لإخوانهم الذين كفروا من أهل الكتاب, باللغة نيانجا

﴿ألم تر إلى الذين نافقوا يقولون لإخوانهم الذين كفروا من أهل الكتاب﴾ [الحَشر: 11]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi wawaona amene achita uchiphamaso? Amene akunena kwa anzawo amene sadakhulupirire pakati pa anthu a mabuku: “Ndithu ngati (mukakamizidwa) kutuluka mu mzinda wa Madina, ndithudi tidzatuluka nanu pamodzi ndipo sitingamvere aliyense za inu mpaka muyaya; ngati mutamenyedwa nkhondo (ndi Asilamu) tidzakuthandizani. Koma Allah akuikira umboni kuti iwo ndionama (pa zimene alonjeza)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek