×

Ndipo iwo ndi amene, awa asadadze, adali ndi nyumba zawo ndipo adalowa 59:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hashr ⮕ (59:9) ayat 9 in Chichewa

59:9 Surah Al-hashr ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 9 - الحَشر - Page - Juz 28

﴿وَٱلَّذِينَ تَبَوَّءُو ٱلدَّارَ وَٱلۡإِيمَٰنَ مِن قَبۡلِهِمۡ يُحِبُّونَ مَنۡ هَاجَرَ إِلَيۡهِمۡ وَلَا يَجِدُونَ فِي صُدُورِهِمۡ حَاجَةٗ مِّمَّآ أُوتُواْ وَيُؤۡثِرُونَ عَلَىٰٓ أَنفُسِهِمۡ وَلَوۡ كَانَ بِهِمۡ خَصَاصَةٞۚ وَمَن يُوقَ شُحَّ نَفۡسِهِۦ فَأُوْلَٰٓئِكَ هُمُ ٱلۡمُفۡلِحُونَ ﴾
[الحَشر: 9]

Ndipo iwo ndi amene, awa asadadze, adali ndi nyumba zawo ndipo adalowa Chisilamu, ndipo adaonetsa chikondi kwa iwo amene amadza kwa iwo, ndipo samachita kaduka ndi katundu amene aperekedwa kwa iwo koma amalolera kuti iwo akhale otsiliza polandira ngakhale kuti nawonso amazifuna. Ndipo aliyense amene amadziteteza ku zilakolako zake, ndithudi, iye adzakhala opambana

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين تبوءوا الدار والإيمان من قبلهم يحبون من هاجر إليهم ولا يجدون, باللغة نيانجا

﴿والذين تبوءوا الدار والإيمان من قبلهم يحبون من هاجر إليهم ولا يجدون﴾ [الحَشر: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma amene adakhala kale mu mzinda uwu (wa Madina) ndi kukhulupirira akukonda amene adasamukira kwa iwo. Ndipo sakupeza vuto m’mitima mwawo pa zimene anzawo apatsidwa, ndipo akutsogoza zofuna za anzawo pa zawo, ngakhale iwo akuzifunitsitsa. Ndipo amene atetezedwa (ndi Allah) ku umbombo wa mitima yawo, amenewo ndiwo opambana
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek