×

Chifukwa iwo adatsutsa Mulungu ndi Mtumwi mwake. Ndipo ngati wina atsutsa Mulungu 59:4 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hashr ⮕ (59:4) ayat 4 in Chichewa

59:4 Surah Al-hashr ayat 4 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 4 - الحَشر - Page - Juz 28

﴿ذَٰلِكَ بِأَنَّهُمۡ شَآقُّواْ ٱللَّهَ وَرَسُولَهُۥۖ وَمَن يُشَآقِّ ٱللَّهَ فَإِنَّ ٱللَّهَ شَدِيدُ ٱلۡعِقَابِ ﴾
[الحَشر: 4]

Chifukwa iwo adatsutsa Mulungu ndi Mtumwi mwake. Ndipo ngati wina atsutsa Mulungu ndi Mtumwi wake, ndithudi, Mulungu ali ndi chilango choopsa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ذلك بأنهم شاقوا الله ورسوله ومن يشاق الله فإن الله شديد العقاب, باللغة نيانجا

﴿ذلك بأنهم شاقوا الله ورسوله ومن يشاق الله فإن الله شديد العقاب﴾ [الحَشر: 4]

Khaled Ibrahim Betala
“Zimenezo nchifukwa chakuti iwo adamtsutsa Allah ndi Mthenga Wake, (kutsutsa kopyola muyeso); ndipo amene akutsutsa Allah (sangapulumuke ku chilango Chake). Ndithu Allah Ndiwolanga mwaukali
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek