Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 5 - الحَشر - Page - Juz 28
﴿مَا قَطَعۡتُم مِّن لِّينَةٍ أَوۡ تَرَكۡتُمُوهَا قَآئِمَةً عَلَىٰٓ أُصُولِهَا فَبِإِذۡنِ ٱللَّهِ وَلِيُخۡزِيَ ٱلۡفَٰسِقِينَ ﴾
[الحَشر: 5]
﴿ما قطعتم من لينة أو تركتموها قائمة على أصولها فبإذن الله وليخزي﴾ [الحَشر: 5]
Khaled Ibrahim Betala “Sim’dadule mtengo uliwonse wa zipatso za kanjedza, (inu Asilamu), kapena kuusiya uli chiimire ndi thunthu lake koma nchifuniro cha Allah ndi kuti awayalutse otuluka m’malamulo Ake |