×

Ngati Mulungu akadapanda kuwalamulira kuti achotsedwe, ndithudi, Iye akanawalanga m’dziko lomwe lino 59:3 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hashr ⮕ (59:3) ayat 3 in Chichewa

59:3 Surah Al-hashr ayat 3 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 3 - الحَشر - Page - Juz 28

﴿وَلَوۡلَآ أَن كَتَبَ ٱللَّهُ عَلَيۡهِمُ ٱلۡجَلَآءَ لَعَذَّبَهُمۡ فِي ٱلدُّنۡيَاۖ وَلَهُمۡ فِي ٱلۡأٓخِرَةِ عَذَابُ ٱلنَّارِ ﴾
[الحَشر: 3]

Ngati Mulungu akadapanda kuwalamulira kuti achotsedwe, ndithudi, Iye akanawalanga m’dziko lomwe lino ndipo m’moyo umene uli nkudza, ndithudi, iwo adzalandira chilango cha ku Gahena

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولولا أن كتب الله عليهم الجلاء لعذبهم في الدنيا ولهم في الآخرة, باللغة نيانجا

﴿ولولا أن كتب الله عليهم الجلاء لعذبهم في الدنيا ولهم في الآخرة﴾ [الحَشر: 3]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo kukadapanda kuti Allah adawalembera (pachiyambi) kusamuka (m’nyumba zawo), akadawalanga pa dziko pompano; koma chilango cha Moto chili pa iwo tsiku lachimaliziro
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek