×

Ndipo, ndithudi, Atumwi ena adasekedwa iwe usadadze, koma amene anali kuwaseka anazungulilidwa 6:10 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-An‘am ⮕ (6:10) ayat 10 in Chichewa

6:10 Surah Al-An‘am ayat 10 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 10 - الأنعَام - Page - Juz 7

﴿وَلَقَدِ ٱسۡتُهۡزِئَ بِرُسُلٖ مِّن قَبۡلِكَ فَحَاقَ بِٱلَّذِينَ سَخِرُواْ مِنۡهُم مَّا كَانُواْ بِهِۦ يَسۡتَهۡزِءُونَ ﴾
[الأنعَام: 10]

Ndipo, ndithudi, Atumwi ena adasekedwa iwe usadadze, koma amene anali kuwaseka anazungulilidwa ndi zinthu zomwe iwo anali kuseka

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد استهزئ برسل من قبلك فحاق بالذين سخروا منهم ما كانوا به, باللغة نيانجا

﴿ولقد استهزئ برسل من قبلك فحاق بالذين سخروا منهم ما كانوا به﴾ [الأنعَام: 10]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi, adachitidwa chipongwe atumiki patsogolo pako; koma (mapeto ake) aja mwa iwo omwe adachita chipongwe zidawazinga zomwe adali kuzichitira chipongwe
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek