×

Ngakhale Ife tikadawatumizira iwo angelo ndi kupangaanthuakufakutialankhulenawondikusonkhanitsa zinthu zonse pamaso pawo, iwo 6:111 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-An‘am ⮕ (6:111) ayat 111 in Chichewa

6:111 Surah Al-An‘am ayat 111 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 111 - الأنعَام - Page - Juz 8

﴿۞ وَلَوۡ أَنَّنَا نَزَّلۡنَآ إِلَيۡهِمُ ٱلۡمَلَٰٓئِكَةَ وَكَلَّمَهُمُ ٱلۡمَوۡتَىٰ وَحَشَرۡنَا عَلَيۡهِمۡ كُلَّ شَيۡءٖ قُبُلٗا مَّا كَانُواْ لِيُؤۡمِنُوٓاْ إِلَّآ أَن يَشَآءَ ٱللَّهُ وَلَٰكِنَّ أَكۡثَرَهُمۡ يَجۡهَلُونَ ﴾
[الأنعَام: 111]

Ngakhale Ife tikadawatumizira iwo angelo ndi kupangaanthuakufakutialankhulenawondikusonkhanitsa zinthu zonse pamaso pawo, iwo sakadakhulupirirabe pokhapokha ngati Mulungu afuna koma ambiri a iwo ndi anthu osadziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولو أننا نـزلنا إليهم الملائكة وكلمهم الموتى وحشرنا عليهم كل شيء قبلا, باللغة نيانجا

﴿ولو أننا نـزلنا إليهم الملائكة وكلمهم الموتى وحشرنا عليهم كل شيء قبلا﴾ [الأنعَام: 111]

Khaled Ibrahim Betala
“۞ Ndipo ngati tikadawatumizira angelo (kuti adzaikire umboni za uneneri wako), ndipo akufa nkuwayankhula, (naonso nkuvomereza kuti izi nzoona; kuonjezera apo) nkuwasonkhanitsira chinthu chilichonse pamaso pawo, sakadakhulupirira pokhapokha Allah akadafuna koma ambiri a iwo sazindikira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek