Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 129 - الأنعَام - Page - Juz 8
﴿وَكَذَٰلِكَ نُوَلِّي بَعۡضَ ٱلظَّٰلِمِينَ بَعۡضَۢا بِمَا كَانُواْ يَكۡسِبُونَ ﴾ 
[الأنعَام: 129]
﴿وكذلك نولي بعض الظالمين بعضا بما كانوا يكسبون﴾ [الأنعَام: 129]
| Khaled Ibrahim Betala “Chomwechi timaika chimvano pakati pawochita zoipa chifukwa cha machimo omwe adali kupeza (kuchokera m’zochita zawo zoipa) |