Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 135 - الأنعَام - Page - Juz 8
﴿قُلۡ يَٰقَوۡمِ ٱعۡمَلُواْ عَلَىٰ مَكَانَتِكُمۡ إِنِّي عَامِلٞۖ فَسَوۡفَ تَعۡلَمُونَ مَن تَكُونُ لَهُۥ عَٰقِبَةُ ٱلدَّارِۚ إِنَّهُۥ لَا يُفۡلِحُ ٱلظَّٰلِمُونَ ﴾
[الأنعَام: 135]
﴿قل ياقوم اعملوا على مكانتكم إني عامل فسوف تعلمون من تكون له﴾ [الأنعَام: 135]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “E inu anthu anga! Chitani zanu (zimene mufuna) momwe mungathere. Nanenso ndichita zanga. Choncho mudzaziwa kuti ndani mapeto ake adzakhale ndi malo abwino. Ndithudi, sangapambane anthu ochita zoipa.” |