Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 156 - الأنعَام - Page - Juz 8
﴿أَن تَقُولُوٓاْ إِنَّمَآ أُنزِلَ ٱلۡكِتَٰبُ عَلَىٰ طَآئِفَتَيۡنِ مِن قَبۡلِنَا وَإِن كُنَّا عَن دِرَاسَتِهِمۡ لَغَٰفِلِينَ ﴾
[الأنعَام: 156]
﴿أن تقولوا إنما أنـزل الكتاب على طائفتين من قبلنا وإن كنا عن﴾ [الأنعَام: 156]
Khaled Ibrahim Betala “Kuti musadzanene (tsiku la Qiyâma) kuti: “Mabuku adavumbulutsidwa pa magulu awiri omwe adalipo patsogolo pathu, (Ayuda ndi Akhrisitu); ndipo ife sitidadziwe chilichonse pa zomwe adali kuwerenga ndi kuphunzira.” |