×

Ndithudi Ife tidatumiza, iwe usanadze, Atumwi ku mitundu ina. Ndipo tidawagwetsera umphawi, 6:42 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-An‘am ⮕ (6:42) ayat 42 in Chichewa

6:42 Surah Al-An‘am ayat 42 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 42 - الأنعَام - Page - Juz 7

﴿وَلَقَدۡ أَرۡسَلۡنَآ إِلَىٰٓ أُمَمٖ مِّن قَبۡلِكَ فَأَخَذۡنَٰهُم بِٱلۡبَأۡسَآءِ وَٱلضَّرَّآءِ لَعَلَّهُمۡ يَتَضَرَّعُونَ ﴾
[الأنعَام: 42]

Ndithudi Ife tidatumiza, iwe usanadze, Atumwi ku mitundu ina. Ndipo tidawagwetsera umphawi, matenda ndi matsoka ochuluka kuti akhoza kukhulupilira modzichepetsa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد أرسلنا إلى أمم من قبلك فأخذناهم بالبأساء والضراء لعلهم يتضرعون, باللغة نيانجا

﴿ولقد أرسلنا إلى أمم من قبلك فأخذناهم بالبأساء والضراء لعلهم يتضرعون﴾ [الأنعَام: 42]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu tidawatumiza (atumiki) ku mibadwo yomwe idalipo iwe usadadze. Ndipo tidaikhaulitsa (mibadwoyo) ndi mazunzo ndi masautso kuti iyo idzichepetse (pambuyo podzikuza)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek