×

Nena, “Ine ndaletsedwa kupembedza milungu imene inumumaipembedzapowonjezerapa Mulungu.” Nena,“Ine sindidzatsatira zilakolako zanu 6:56 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-An‘am ⮕ (6:56) ayat 56 in Chichewa

6:56 Surah Al-An‘am ayat 56 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 56 - الأنعَام - Page - Juz 7

﴿قُلۡ إِنِّي نُهِيتُ أَنۡ أَعۡبُدَ ٱلَّذِينَ تَدۡعُونَ مِن دُونِ ٱللَّهِۚ قُل لَّآ أَتَّبِعُ أَهۡوَآءَكُمۡ قَدۡ ضَلَلۡتُ إِذٗا وَمَآ أَنَا۠ مِنَ ٱلۡمُهۡتَدِينَ ﴾
[الأنعَام: 56]

Nena, “Ine ndaletsedwa kupembedza milungu imene inumumaipembedzapowonjezerapa Mulungu.” Nena,“Ine sindidzatsatira zilakolako zanu zachabe. Ngati nditatero ndiye kuti ndasochera ndipo ine sindikhala mugulu la anthu otsogozedwa bwino.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل إني نهيت أن أعبد الذين تدعون من دون الله قل لا, باللغة نيانجا

﴿قل إني نهيت أن أعبد الذين تدعون من دون الله قل لا﴾ [الأنعَام: 56]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Ndithu ine ndaletsedwa kupembedza amene mukuwapembedza kusiya Allah.” Nena: “Sinditsata zilakolako zanu; ndikadatero ndikadasokera ndipo sindikadakhala mwa owongoka.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek