Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 55 - الأنعَام - Page - Juz 7
﴿وَكَذَٰلِكَ نُفَصِّلُ ٱلۡأٓيَٰتِ وَلِتَسۡتَبِينَ سَبِيلُ ٱلۡمُجۡرِمِينَ ﴾ 
[الأنعَام: 55]
﴿وكذلك نفصل الآيات ولتستبين سبيل المجرمين﴾ [الأنعَام: 55]
| Khaled Ibrahim Betala “Mmenemo ndi momwe tikufotokozera zizindikiro mwatsatanetsatane (kuti choonadi chioneke) ndi kuti njira ya oipa idziwike bwinobwino |