×

Oh iwe Mtumwi! Ngati akazi okhulupirira adza kwa iwe kudzalumbira lonjezo lakuti 60:12 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mumtahanah ⮕ (60:12) ayat 12 in Chichewa

60:12 Surah Al-Mumtahanah ayat 12 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mumtahanah ayat 12 - المُمتَحنَة - Page - Juz 28

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلنَّبِيُّ إِذَا جَآءَكَ ٱلۡمُؤۡمِنَٰتُ يُبَايِعۡنَكَ عَلَىٰٓ أَن لَّا يُشۡرِكۡنَ بِٱللَّهِ شَيۡـٔٗا وَلَا يَسۡرِقۡنَ وَلَا يَزۡنِينَ وَلَا يَقۡتُلۡنَ أَوۡلَٰدَهُنَّ وَلَا يَأۡتِينَ بِبُهۡتَٰنٖ يَفۡتَرِينَهُۥ بَيۡنَ أَيۡدِيهِنَّ وَأَرۡجُلِهِنَّ وَلَا يَعۡصِينَكَ فِي مَعۡرُوفٖ فَبَايِعۡهُنَّ وَٱسۡتَغۡفِرۡ لَهُنَّ ٱللَّهَۚ إِنَّ ٱللَّهَ غَفُورٞ رَّحِيمٞ ﴾
[المُمتَحنَة: 12]

Oh iwe Mtumwi! Ngati akazi okhulupirira adza kwa iwe kudzalumbira lonjezo lakuti sadzamufanizira Mulungu ndi wina wake akamapembedza, kuti sadzaba, sadzachita chigololo, sadzapha ana awo, sadzalankhula mawu ojeda, sadzapeka nkhani zabodza ndipo kuti adzakumvera iwe pa nkhani ina iliyonse, iwe uyenera kulandira lonjezo lawo ndipo pempha kwa Mulungu kuti awakhululukire machimo awo chifukwa Mulungu ndi wokhululukira ndi Mwini chisoni chosatha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها النبي إذا جاءك المؤمنات يبايعنك على أن لا يشركن بالله شيئا, باللغة نيانجا

﴿ياأيها النبي إذا جاءك المؤمنات يبايعنك على أن لا يشركن بالله شيئا﴾ [المُمتَحنَة: 12]

Khaled Ibrahim Betala
“E iwe Mtumiki! Akakudzera akazi okhulupirira kudzakulonjeza kuti samphatikiza Allah ndi chilichonse ndi kuti saziba, sazichita chiwerewere, sazipha ana awo ndi kuti sazinena bodza lamkunkhuniza, lomwe akulipeka pakati pa manja awo ndi miyendo yawo (pompachika mwana kwa wina amene sali tate wake), ndi kutinso sadzakunyoza pa chinthu chabwino (chimene ukuwaitanira), landira lonjezo lawolo, ndipo apemphere chikhululuko kwa Allah. Ndithu Allah Ngokhululuka kwambiri, Ngwachisoni
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek