×

Ndipo ngati ena, mwa akazi anu, athawa ndi kukakwatiwa ndi osakhulupirira, ndipo 60:11 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mumtahanah ⮕ (60:11) ayat 11 in Chichewa

60:11 Surah Al-Mumtahanah ayat 11 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mumtahanah ayat 11 - المُمتَحنَة - Page - Juz 28

﴿وَإِن فَاتَكُمۡ شَيۡءٞ مِّنۡ أَزۡوَٰجِكُمۡ إِلَى ٱلۡكُفَّارِ فَعَاقَبۡتُمۡ فَـَٔاتُواْ ٱلَّذِينَ ذَهَبَتۡ أَزۡوَٰجُهُم مِّثۡلَ مَآ أَنفَقُواْۚ وَٱتَّقُواْ ٱللَّهَ ٱلَّذِيٓ أَنتُم بِهِۦ مُؤۡمِنُونَ ﴾
[المُمتَحنَة: 11]

Ndipo ngati ena, mwa akazi anu, athawa ndi kukakwatiwa ndi osakhulupirira, ndipo inu mupeza mwayi wolandira akazi wochokera kwa anthu osakhulupirira abwezereni chiwongo ndi china chilichonse chimene iwo adapereka anthu amene akazi awo awathawa. Ndipo opani Mulungu amene inu mumamukhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن فاتكم شيء من أزواجكم إلى الكفار فعاقبتم فآتوا الذين ذهبت أزواجهم, باللغة نيانجا

﴿وإن فاتكم شيء من أزواجكم إلى الكفار فعاقبتم فآتوا الذين ذهبت أزواجهم﴾ [المُمتَحنَة: 11]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ngati mmodzi mwa akazi anu atakuthawani kupita kwa Akafiri, ndipo (mwadzidzidzi) mwakachita nkhondo (ndi kupeza chuma chosiya adani anu), apatseni amene awathawa akazi awo chofanana ndi chimene adapereka (pokwatira). Ndipo muopeni Allah amene inu mukumkhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek