×

Ndipo Iye adzakupatsani madalitso ena amene mumakonda. Chithandizo chochokera kwa Mulungu ndi 61:13 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah As-saff ⮕ (61:13) ayat 13 in Chichewa

61:13 Surah As-saff ayat 13 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah As-saff ayat 13 - الصَّف - Page - Juz 28

﴿وَأُخۡرَىٰ تُحِبُّونَهَاۖ نَصۡرٞ مِّنَ ٱللَّهِ وَفَتۡحٞ قَرِيبٞۗ وَبَشِّرِ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[الصَّف: 13]

Ndipo Iye adzakupatsani madalitso ena amene mumakonda. Chithandizo chochokera kwa Mulungu ndi kupambana mwamsanga. Kotero auze nkhani yabwino anthu okhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأخرى تحبونها نصر من الله وفتح قريب وبشر المؤمنين, باللغة نيانجا

﴿وأخرى تحبونها نصر من الله وفتح قريب وبشر المؤمنين﴾ [الصَّف: 13]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndizina zomwe mukuzifuna. Thandizo (lonse) lichokera kwa Allah ndi kugonjetsa kumene kuli pafupi; ndipo auze nkhani yabwino okhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek