Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mulk ayat 12 - المُلك - Page - Juz 29
﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ يَخۡشَوۡنَ رَبَّهُم بِٱلۡغَيۡبِ لَهُم مَّغۡفِرَةٞ وَأَجۡرٞ كَبِيرٞ ﴾
[المُلك: 12]
﴿إن الذين يخشون ربهم بالغيب لهم مغفرة وأجر كبير﴾ [المُلك: 12]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithudi amene akumuopa Mbuye wawo pomwe iwo sakumuona, adzapeza chikhululuko pa machimo awo ndi malipiro aakulu (pa zabwino zomwe ankachita) |