Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mulk ayat 16 - المُلك - Page - Juz 29
﴿ءَأَمِنتُم مَّن فِي ٱلسَّمَآءِ أَن يَخۡسِفَ بِكُمُ ٱلۡأَرۡضَ فَإِذَا هِيَ تَمُورُ ﴾
[المُلك: 16]
﴿أأمنتم من في السماء أن يخسف بكم الأرض فإذا هي تمور﴾ [المُلك: 16]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi muli m’chitetezo kwa Amene ali kumwamba kuti sangakukwilireni m’nthaka (ndikukudzidzimutsani) pamene nthaka ikugwedezeka molimba |