Quran with Chichewa translation - Surah Al-haqqah ayat 50 - الحَاقة - Page - Juz 29
﴿وَإِنَّهُۥ لَحَسۡرَةٌ عَلَى ٱلۡكَٰفِرِينَ ﴾
[الحَاقة: 50]
﴿وإنه لحسرة على الكافرين﴾ [الحَاقة: 50]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu iyi (Qur’an) idzakhala chowadandaulitsa (chachikulu) osakhulupirira (pamene adzaona chilango chawo ndi mtendere wa okhulupirira) |