×

Ndithudi ine sindidzanena china chilichonse chokhudza Mulungu kupatula choonadi. Ndithudi ine ndakubweretserani 7:105 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:105) ayat 105 in Chichewa

7:105 Surah Al-A‘raf ayat 105 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 105 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿حَقِيقٌ عَلَىٰٓ أَن لَّآ أَقُولَ عَلَى ٱللَّهِ إِلَّا ٱلۡحَقَّۚ قَدۡ جِئۡتُكُم بِبَيِّنَةٖ مِّن رَّبِّكُمۡ فَأَرۡسِلۡ مَعِيَ بَنِيٓ إِسۡرَٰٓءِيلَ ﴾
[الأعرَاف: 105]

Ndithudi ine sindidzanena china chilichonse chokhudza Mulungu kupatula choonadi. Ndithudi ine ndakubweretserani chizindikiro chosakaikitsa kuchokera kwa Ambuye wanu. Motero alole ana a Israyeli kuti apite ndi ine.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: حقيق على أن لا أقول على الله إلا الحق قد جئتكم ببينة, باللغة نيانجا

﴿حقيق على أن لا أقول على الله إلا الحق قد جئتكم ببينة﴾ [الأعرَاف: 105]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndikofunika kwa ine kuti ndisamnenere Allah chilichonse koma choonadi basi. Ndithu ndakudzerani ndi chizindikiro choonekera kuchokera kwa Mbuye wanu. Choncho, aleke ndinke nawo ana a Israyeli.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek