Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 111 - الأعرَاف - Page - Juz 9
﴿قَالُوٓاْ أَرۡجِهۡ وَأَخَاهُ وَأَرۡسِلۡ فِي ٱلۡمَدَآئِنِ حَٰشِرِينَ ﴾
[الأعرَاف: 111]
﴿قالوا أرجه وأخاه وأرسل في المدائن حاشرين﴾ [الأعرَاف: 111]
Khaled Ibrahim Betala “(Iwo) adati (kwa Farawo): “Muleke pang’ono iye ndi m’bale wakeyu (usawaphe); ndipo tumiza osonkhanitsa m’mizinda kuti akusonkhanitsire (amatsenga onse akuluakulu).” |