×

“Ndipo inu mufuna kubwezera kwa ife chifukwa cha kuti takhulupirira mu zizindikiro 7:126 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:126) ayat 126 in Chichewa

7:126 Surah Al-A‘raf ayat 126 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 126 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿وَمَا تَنقِمُ مِنَّآ إِلَّآ أَنۡ ءَامَنَّا بِـَٔايَٰتِ رَبِّنَا لَمَّا جَآءَتۡنَاۚ رَبَّنَآ أَفۡرِغۡ عَلَيۡنَا صَبۡرٗا وَتَوَفَّنَا مُسۡلِمِينَ ﴾
[الأعرَاف: 126]

“Ndipo inu mufuna kubwezera kwa ife chifukwa cha kuti takhulupirira mu zizindikiro za Ambuye wathu pamene zalangizidwa kwa ife! Ambuye wathu! Tipatseni kupirira ndipo konzani kuti ife tife ngati Asilamu.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما تنقم منا إلا أن آمنا بآيات ربنا لما جاءتنا ربنا أفرغ, باللغة نيانجا

﴿وما تنقم منا إلا أن آمنا بآيات ربنا لما جاءتنا ربنا أفرغ﴾ [الأعرَاف: 126]

Khaled Ibrahim Betala
““Komatu palibe choipa chimene waona mwa ife kupatula kuti takhulupirira zizindikiro za Mbuye wathu pamene zatidzera. E Mbuye wathu! Titsanulireni chipiliro, ndipo tipatseni imfa uku tili Asilamu (ogonjera Inu).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek