×

Mafumu a anthu a Farao adati: “Kodi inu mukumusiya Mose ndi anthu 7:127 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:127) ayat 127 in Chichewa

7:127 Surah Al-A‘raf ayat 127 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 127 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿وَقَالَ ٱلۡمَلَأُ مِن قَوۡمِ فِرۡعَوۡنَ أَتَذَرُ مُوسَىٰ وَقَوۡمَهُۥ لِيُفۡسِدُواْ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَيَذَرَكَ وَءَالِهَتَكَۚ قَالَ سَنُقَتِّلُ أَبۡنَآءَهُمۡ وَنَسۡتَحۡيِۦ نِسَآءَهُمۡ وَإِنَّا فَوۡقَهُمۡ قَٰهِرُونَ ﴾
[الأعرَاف: 127]

Mafumu a anthu a Farao adati: “Kodi inu mukumusiya Mose ndi anthu ake kuti azichita zoipa m’dziko ndi kukusiya iwe ndi milungu yako?” Iye adayankha, “Ife tidzapha ana awo amuna ndi kusiya ana awo akazi ndi moyo ndipo Ife ndithudi tili ndi mphamvu pa iwo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقال الملأ من قوم فرعون أتذر موسى وقومه ليفسدوا في الأرض ويذرك, باللغة نيانجا

﴿وقال الملأ من قوم فرعون أتذر موسى وقومه ليفسدوا في الأرض ويذرك﴾ [الأعرَاف: 127]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo nduna za mwa anthu a Farawo zidati (kwa Farawo): “Kodi umuleka Mûsa ndi anthu ake kuti abwere ndi chisokonezo m’dziko, ndi kuti akusiye iwe ndi milungu yako (yomwe adatilangiza makolo athu kuti tipembedze pamodzi ndi iwe)? (Farawo) Adati: “Tipha ana awo achimuna ndikuwasiya amoyo (ana awo) achikazi. Ndithudi ife pa iwo tili ndi mphamvu zowagonjetsera.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek