×

Ndipo Ife tidawapatsa anthu amene amati ndi ofooka ulamuliro wa maiko a 7:137 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:137) ayat 137 in Chichewa

7:137 Surah Al-A‘raf ayat 137 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 137 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿وَأَوۡرَثۡنَا ٱلۡقَوۡمَ ٱلَّذِينَ كَانُواْ يُسۡتَضۡعَفُونَ مَشَٰرِقَ ٱلۡأَرۡضِ وَمَغَٰرِبَهَا ٱلَّتِي بَٰرَكۡنَا فِيهَاۖ وَتَمَّتۡ كَلِمَتُ رَبِّكَ ٱلۡحُسۡنَىٰ عَلَىٰ بَنِيٓ إِسۡرَٰٓءِيلَ بِمَا صَبَرُواْۖ وَدَمَّرۡنَا مَا كَانَ يَصۡنَعُ فِرۡعَوۡنُ وَقَوۡمُهُۥ وَمَا كَانُواْ يَعۡرِشُونَ ﴾
[الأعرَاف: 137]

Ndipo Ife tidawapatsa anthu amene amati ndi ofooka ulamuliro wa maiko a ku m’mawa ndi ku madzulo, amene tidawadalitsa. Ndipo Mau olemekezeka Ambuye wako kwa ana a Israyeli, adakwaniritsidwa chifukwa cha kupirira kwawo. Ndipo Ife tidaononga zinthu zonse zomwe Farao ndi anthu ake adapanga ndi zimene anali kumanga

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأورثنا القوم الذين كانوا يستضعفون مشارق الأرض ومغاربها التي باركنا فيها وتمت, باللغة نيانجا

﴿وأورثنا القوم الذين كانوا يستضعفون مشارق الأرض ومغاربها التي باركنا فيها وتمت﴾ [الأعرَاف: 137]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo anthu omwe adali kuponderezedwa tidawachita kukhala amlowammalo a kuvuma kwa dziko ndi kuzambwe kwake, lomwe tidaikamo madalitso (ambiri). Ndipo mawu abwino a Mbuye wako adakwaniritsidwa kwa ana a Israyeli chifukwa cha kupirira kwawo (pa zomwe adakumana nazo). Ndipo tidazigumula ndi kuziononga zomwe Farawo ndi anthu ake ankapanga ndi zomwe ankamanga
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek