×

Koma anthu oipa amene adali pakati pawo, adasintha mawu amene adapatsidwa, motero 7:162 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:162) ayat 162 in Chichewa

7:162 Surah Al-A‘raf ayat 162 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 162 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿فَبَدَّلَ ٱلَّذِينَ ظَلَمُواْ مِنۡهُمۡ قَوۡلًا غَيۡرَ ٱلَّذِي قِيلَ لَهُمۡ فَأَرۡسَلۡنَا عَلَيۡهِمۡ رِجۡزٗا مِّنَ ٱلسَّمَآءِ بِمَا كَانُواْ يَظۡلِمُونَ ﴾
[الأعرَاف: 162]

Koma anthu oipa amene adali pakati pawo, adasintha mawu amene adapatsidwa, motero Ife tidawatumizira chilango kuchokera kumwamba chifukwa cha kulakwa kwawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فبدل الذين ظلموا منهم قولا غير الذي قيل لهم فأرسلنا عليهم رجزا, باللغة نيانجا

﴿فبدل الذين ظلموا منهم قولا غير الذي قيل لهم فأرسلنا عليهم رجزا﴾ [الأعرَاف: 162]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma aja amene adadzichitira okha zoipa, mwa iwo adasintha mawu ena kusiya omwe adauzidwa; choncho, tidawatumizira chilango chochokera kumwamba chifukwa chodzichitira okha zoipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek