×

Akakhala iwo amene amatsatira moona Mau a Mulungu ndi kupitiriza mapemphero, ndithudi, 7:170 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:170) ayat 170 in Chichewa

7:170 Surah Al-A‘raf ayat 170 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 170 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿وَٱلَّذِينَ يُمَسِّكُونَ بِٱلۡكِتَٰبِ وَأَقَامُواْ ٱلصَّلَوٰةَ إِنَّا لَا نُضِيعُ أَجۡرَ ٱلۡمُصۡلِحِينَ ﴾
[الأعرَاف: 170]

Akakhala iwo amene amatsatira moona Mau a Mulungu ndi kupitiriza mapemphero, ndithudi, Ife sitidzaononga mphotho za anthu ochita ntchito zabwino

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين يمسكون بالكتاب وأقاموا الصلاة إنا لا نضيع أجر المصلحين, باللغة نيانجا

﴿والذين يمسكون بالكتاب وأقاموا الصلاة إنا لا نضيع أجر المصلحين﴾ [الأعرَاف: 170]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene akugwirisitsa buku (la Allah potsata zophunzitsa zake) ndi kumapemphera Swala, (tidzawalipira zabwino). Ndithu Ife sitipititsa pachabe malipiro a ochita zabwino
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek