×

Mulungu ali ndi mayina abwino kwambiri. Motero muitaneni pa mayina amenewo ndipo 7:180 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:180) ayat 180 in Chichewa

7:180 Surah Al-A‘raf ayat 180 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 180 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿وَلِلَّهِ ٱلۡأَسۡمَآءُ ٱلۡحُسۡنَىٰ فَٱدۡعُوهُ بِهَاۖ وَذَرُواْ ٱلَّذِينَ يُلۡحِدُونَ فِيٓ أَسۡمَٰٓئِهِۦۚ سَيُجۡزَوۡنَ مَا كَانُواْ يَعۡمَلُونَ ﴾
[الأعرَاف: 180]

Mulungu ali ndi mayina abwino kwambiri. Motero muitaneni pa mayina amenewo ndipo asiyeni iwo amene amaononga ulemerero wa mayina ake. Iwo adzalangidwa chifukwa cha zimene adali kuchita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولله الأسماء الحسنى فادعوه بها وذروا الذين يلحدون في أسمائه سيجزون ما, باللغة نيانجا

﴿ولله الأسماء الحسنى فادعوه بها وذروا الذين يلحدون في أسمائه سيجزون ما﴾ [الأعرَاف: 180]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo Allah ali nawo maina abwino. Choncho, muitaneni ndi mainawo. Alekeni amene akupotoza maina Ake posachedwapa alipidwa zomwe akhala akuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek