×

oh inu ana a Adamu! Ngati Atumwi a mtundu wanu adzadza kwa 7:35 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:35) ayat 35 in Chichewa

7:35 Surah Al-A‘raf ayat 35 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 35 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿يَٰبَنِيٓ ءَادَمَ إِمَّا يَأۡتِيَنَّكُمۡ رُسُلٞ مِّنكُمۡ يَقُصُّونَ عَلَيۡكُمۡ ءَايَٰتِي فَمَنِ ٱتَّقَىٰ وَأَصۡلَحَ فَلَا خَوۡفٌ عَلَيۡهِمۡ وَلَا هُمۡ يَحۡزَنُونَ ﴾
[الأعرَاف: 35]

oh inu ana a Adamu! Ngati Atumwi a mtundu wanu adzadza kwa inu kudzakulalikirani chivumbulutso changa ndipo aliyense amene akhala olungama ndi kumachita zabwino, iwo sadzaopa china chilichonse kapena kuda nkhawa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يابني آدم إما يأتينكم رسل منكم يقصون عليكم آياتي فمن اتقى وأصلح, باللغة نيانجا

﴿يابني آدم إما يأتينكم رسل منكم يقصون عليكم آياتي فمن اتقى وأصلح﴾ [الأعرَاف: 35]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu ana a Adam! Akakudzerani Atumiki ochokera mwa inu namakuuzani zivumbulutso Zanga, (avomereni), choncho omwe adzitchinjiriza ku zoletsedwa ndi kuchita zabwino, sipadzakhala mantha pa iwo ndiponso sadzadandaula
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek