×

Atsogoleri a anthu osakhulupirira ochokera ku mtundu wa Hudadati:“Ifetilikukuonakutiiwendiwewopusandipo ife tili kuganiza 7:66 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:66) ayat 66 in Chichewa

7:66 Surah Al-A‘raf ayat 66 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 66 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿قَالَ ٱلۡمَلَأُ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ مِن قَوۡمِهِۦٓ إِنَّا لَنَرَىٰكَ فِي سَفَاهَةٖ وَإِنَّا لَنَظُنُّكَ مِنَ ٱلۡكَٰذِبِينَ ﴾
[الأعرَاف: 66]

Atsogoleri a anthu osakhulupirira ochokera ku mtundu wa Hudadati:“Ifetilikukuonakutiiwendiwewopusandipo ife tili kuganiza kuti ndiwe mmodzi wa anthu a bodza.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال الملأ الذين كفروا من قومه إنا لنراك في سفاهة وإنا لنظنك, باللغة نيانجا

﴿قال الملأ الذين كفروا من قومه إنا لنراك في سفاهة وإنا لنظنك﴾ [الأعرَاف: 66]

Khaled Ibrahim Betala
“Akuluakulu a mwa anthu ake omwe sadakhulupirire adanena: “Ife tili kukuona kuti uli mu uchidzete, ndipo ife tikukuganizira kuti ndiwe m’modzi wa a bodza.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek