Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 80 - الأعرَاف - Page - Juz 8
﴿وَلُوطًا إِذۡ قَالَ لِقَوۡمِهِۦٓ أَتَأۡتُونَ ٱلۡفَٰحِشَةَ مَا سَبَقَكُم بِهَا مِنۡ أَحَدٖ مِّنَ ٱلۡعَٰلَمِينَ ﴾
[الأعرَاف: 80]
﴿ولوطا إذ قال لقومه أتأتون الفاحشة ما سبقكم بها من أحد من﴾ [الأعرَاف: 80]
Khaled Ibrahim Betala “Nayenso Luti (tidamtuma, ndipo kumbuka) pamene adati kwa anthu ake: “Kodi mukuchita chonyansa chomwe sadakutsogolereni aliyense kuchichita mwa anthu akale m’zolengedwa zonse?” |