×

Motero Saleh adachoka nati, “oh anthu anga! Ine, ndithudi, ndapereka uthenga wa 7:79 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:79) ayat 79 in Chichewa

7:79 Surah Al-A‘raf ayat 79 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 79 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿فَتَوَلَّىٰ عَنۡهُمۡ وَقَالَ يَٰقَوۡمِ لَقَدۡ أَبۡلَغۡتُكُمۡ رِسَالَةَ رَبِّي وَنَصَحۡتُ لَكُمۡ وَلَٰكِن لَّا تُحِبُّونَ ٱلنَّٰصِحِينَ ﴾
[الأعرَاف: 79]

Motero Saleh adachoka nati, “oh anthu anga! Ine, ndithudi, ndapereka uthenga wa Ambuye wanga ndipo ndakupatsani chilangizo chabwino koma inu simukonda anthu okuchenjezani.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فتولى عنهم وقال ياقوم لقد أبلغتكم رسالة ربي ونصحت لكم ولكن لا, باللغة نيانجا

﴿فتولى عنهم وقال ياقوم لقد أبلغتكم رسالة ربي ونصحت لكم ولكن لا﴾ [الأعرَاف: 79]

Khaled Ibrahim Betala
“Tero, Swalih adawasiya (nkupita kwina kwake) uku akunena: “E anthu anga! Ndidafikitsadi uthenga wa Mbuye wanga kwa inu. Ndipo Ndidakuchenjezani ndi kukulangizani. Koma inu simufuna alangizi.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek