Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 83 - الأعرَاف - Page - Juz 8
﴿فَأَنجَيۡنَٰهُ وَأَهۡلَهُۥٓ إِلَّا ٱمۡرَأَتَهُۥ كَانَتۡ مِنَ ٱلۡغَٰبِرِينَ ﴾
[الأعرَاف: 83]
﴿فأنجيناه وأهله إلا امرأته كانت من الغابرين﴾ [الأعرَاف: 83]
Khaled Ibrahim Betala “Koma tidampulumutsa iye ndi banja lake, kupatula mkazi wake; adali m’gulu la otsalira m’mbuyo (adaonongeka) |