Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 82 - الأعرَاف - Page - Juz 8
﴿وَمَا كَانَ جَوَابَ قَوۡمِهِۦٓ إِلَّآ أَن قَالُوٓاْ أَخۡرِجُوهُم مِّن قَرۡيَتِكُمۡۖ إِنَّهُمۡ أُنَاسٞ يَتَطَهَّرُونَ ﴾
[الأعرَاف: 82]
﴿وما كان جواب قومه إلا أن قالوا أخرجوهم من قريتكم إنهم أناس﴾ [الأعرَاف: 82]
Khaled Ibrahim Betala “Kuyankha kwa anthu ake sikudali kwa mtundu wina koma kuti: “Apirikitseni m’mudzi wanu. Ndithu iwowo ndi anthu odziyeretsa. (Choncho akhaliranji m’mudzi wa uve? Akakhale ndi anzawo ochita zaukhondo).” |