Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 97 - الأعرَاف - Page - Juz 9
﴿أَفَأَمِنَ أَهۡلُ ٱلۡقُرَىٰٓ أَن يَأۡتِيَهُم بَأۡسُنَا بَيَٰتٗا وَهُمۡ نَآئِمُونَ ﴾
[الأعرَاف: 97]
﴿أفأمن أهل القرى أن يأتيهم بأسنا بياتا وهم نائمون﴾ [الأعرَاف: 97]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi anthu a m’mizinda (iyo momwe muli anthu oipa) ali ndi chitetezo cholimba kuti chilango chathu sichingawadzere usiku iwo ali mtulo |