×

Ndipo anthu a m’Mizinda imeneyi akadakhulupirira ndi kuopa uchimo, tikadawatsegulira madalitso kuchokera 7:96 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:96) ayat 96 in Chichewa

7:96 Surah Al-A‘raf ayat 96 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 96 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿وَلَوۡ أَنَّ أَهۡلَ ٱلۡقُرَىٰٓ ءَامَنُواْ وَٱتَّقَوۡاْ لَفَتَحۡنَا عَلَيۡهِم بَرَكَٰتٖ مِّنَ ٱلسَّمَآءِ وَٱلۡأَرۡضِ وَلَٰكِن كَذَّبُواْ فَأَخَذۡنَٰهُم بِمَا كَانُواْ يَكۡسِبُونَ ﴾
[الأعرَاف: 96]

Ndipo anthu a m’Mizinda imeneyi akadakhulupirira ndi kuopa uchimo, tikadawatsegulira madalitso kuchokera kumwamba ndi padziko lapansi. Koma iwo adakana choonadi. Motero Ife tidawalanga chifukwa cha zimene adali kuchita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولو أن أهل القرى آمنوا واتقوا لفتحنا عليهم بركات من السماء والأرض, باللغة نيانجا

﴿ولو أن أهل القرى آمنوا واتقوا لفتحنا عليهم بركات من السماء والأرض﴾ [الأعرَاف: 96]

Khaled Ibrahim Betala
“Chikhala kuti eni midziwo adakhulupirira naopa (Allah pamene aneneri adawadzera), tikadawatsekulira madalitso ochokera kumwamba ndi pansi. Koma adatsutsa (aneneri) ndipo tidawaononga chifukwa cha zoipa zomwe ankachita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek